Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 25:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Chipilala chilichonse kutalika kwake chinali mikono 18,+ ndipo mutu+ wake unali wamkuwa. Mutuwo kutalika kwake kunali mikono itatu, ndipo maukonde ndi makangaza*+ amene anazungulira mutuwo, onse anali amkuwa. Chipilala chachiwiri chinalinso ndi maukonde ofanana ndi amenewa.

  • 2 Mbiri 3:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Atatero anapanganso matcheni+ okhala ngati ovala m’khosi ndi kuwaika kumutu kwa zipilala zija, ndipo anapanga makangaza*+ 100 n’kuwaika kumatcheniwo.

  • 2 Mbiri 4:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Anapanganso makangaza 400+ oika pamaukonde awiri aja, mizere iwiri ya makangaza pa ukonde uliwonse. Makangazawo anali okutira mitu iwiri yozungulira imene inali pazipilala ziwiri zija.+

  • Yeremiya 52:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Makangaza amene anali m’mbali mwa zipilalazo analipo 96, ndipo makangaza onse amene anali pamaukondewo analipo 100.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena