1 Mafumu 7:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mitu iwiriyo inali pamwamba pa zipilala, komanso inali pamwamba pa mimba imene inagundana ndi maukonde. Kuzungulira mutu uliwonse, panali makangaza 200+ amene anali m’mizere. Yeremiya 52:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Makangaza amene anali m’mbali mwa zipilalazo analipo 96, ndipo makangaza onse amene anali pamaukondewo analipo 100.+
20 Mitu iwiriyo inali pamwamba pa zipilala, komanso inali pamwamba pa mimba imene inagundana ndi maukonde. Kuzungulira mutu uliwonse, panali makangaza 200+ amene anali m’mizere.
23 Makangaza amene anali m’mbali mwa zipilalazo analipo 96, ndipo makangaza onse amene anali pamaukondewo analipo 100.+