Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 7:42
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Anapanganso makangaza 400+ oika pamaukonde awiri aja, mizere iwiri ya makangaza pa ukonde uliwonse. Makangazawo anali okutira mitu iwiri yooneka ngati mbale zolowa imene inali pazipilala ziwiri zija.

  • Yeremiya 52:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Mutu wa chipilala chilichonse unali wamkuwa.+ Mutuwo kutalika kwake kunali mikono isanu,+ ndipo maukonde ndi makangaza* amene anazungulira mutuwo,+ onse anali amkuwa. Chipilala chachiwiri chinalinso ndi maukonde ofanana ndi amenewa komanso chinali ndi makangaza.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena