2 Mbiri 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno kumaso kwa nyumbayo anamangako zipilala ziwiri+ zazitali mikono 35. Mutu+ wa chipilala chilichonse umene unali pamwamba pake unali wautali mikono isanu.
15 Ndiyeno kumaso kwa nyumbayo anamangako zipilala ziwiri+ zazitali mikono 35. Mutu+ wa chipilala chilichonse umene unali pamwamba pake unali wautali mikono isanu.