2 Mbiri 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kutsogolo kwa nyumbayo anamangako zipilala ziwiri+ zazitali mikono 35. Mutu wa chipilala chilichonse unali wautali mikono 5.+
15 Kutsogolo kwa nyumbayo anamangako zipilala ziwiri+ zazitali mikono 35. Mutu wa chipilala chilichonse unali wautali mikono 5.+