1 Mafumu 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Anapanga mitu iwiri youmba ndi mkuwa+ n’kuiika pamwamba pa zipilalazo. Mutu umodzi kutalika kwake kunali mikono isanu, ndipo mutu winawo kutalika kwake kunalinso mikono isanu.
16 Anapanga mitu iwiri youmba ndi mkuwa+ n’kuiika pamwamba pa zipilalazo. Mutu umodzi kutalika kwake kunali mikono isanu, ndipo mutu winawo kutalika kwake kunalinso mikono isanu.