Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 36:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Anapanganso mizati yake isanu ndi tizitsulo take tokolowekapo nsalu yotchingayo. Mitu ya mizatiyo komanso mfundo zake anazikuta ndi golide. Koma zitsulo zake zisanu zamphako zokhazikapo mizatiyo zinali zamkuwa.+

  • Ekisodo 38:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ndipo zitsulo zokhazikapo nsanamira zinali zamkuwa. Tizitsulo ta nsanamira tokolowekapo nsalu za mpanda ndi tizitsulo tolumikizira tinali tasiliva. Mitu ya nsanamirazo inali yokutidwa ndi siliva, ndipo nsanamira zonse za bwalo zinali ndi tizitsulo tasiliva tolumikizira.+

  • Ekisodo 38:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Masekeli 1,775 asiliva anawagwiritsa ntchito kupangira tizitsulo ta nsanamira tokolowekapo nsalu, ndi kukutira mitu ya nsanamirazo. Atatero analumikiza nsanamirazo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena