1 Mafumu 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako anapanga mizere iwiri ya makangaza* n’kuwazunguliza pamaukonde awiri aja, n’kuveka mitu imene inali pamwamba pa zipilalazo. Anachita zimenezi pamitu+ yonse iwiri. 2 Mbiri 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Atatero anapanganso matcheni+ okhala ngati ovala m’khosi ndi kuwaika kumutu kwa zipilala zija, ndipo anapanga makangaza*+ 100 n’kuwaika kumatcheniwo.
18 Kenako anapanga mizere iwiri ya makangaza* n’kuwazunguliza pamaukonde awiri aja, n’kuveka mitu imene inali pamwamba pa zipilalazo. Anachita zimenezi pamitu+ yonse iwiri.
16 Atatero anapanganso matcheni+ okhala ngati ovala m’khosi ndi kuwaika kumutu kwa zipilala zija, ndipo anapanga makangaza*+ 100 n’kuwaika kumatcheniwo.