2 Mbiri 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anapanganso makangaza 400+ oika pamaukonde awiri aja, mizere iwiri ya makangaza pa ukonde uliwonse. Makangazawo anali okutira mitu iwiri yozungulira imene inali pazipilala ziwiri zija.+
13 Anapanganso makangaza 400+ oika pamaukonde awiri aja, mizere iwiri ya makangaza pa ukonde uliwonse. Makangazawo anali okutira mitu iwiri yozungulira imene inali pazipilala ziwiri zija.+