2 Mbiri 4:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chotero Solomo anapanga ziwiya zimenezi zambirimbiri, moti mkuwawo sunadziwike kulemera kwake.+