Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 7:47
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 47 Solomo sanayeze ziwiya zonse+ chifukwa zinali zochuluka kwambiri.+ Mkuwawo sunadziwike kulemera kwake.+

  • 1 Mbiri 22:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndiyeno Davide anasonkhanitsa zitsulo zambirimbiri zopangira misomali ya zitseko za pazipata komanso zopangira zida zopanira zinthu. Anasonkhanitsanso mkuwa wambirimbiri wosatheka kuuyeza kulemera kwake.+

  • 1 Mbiri 22:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Taona, pa nthawi ya masautso anga+ ndasonkhanitsa golide womangira nyumba ya Yehova wokwanira matalente* 100,000,+ ndi siliva wokwanira matalente 1,000,000. Koma n’zosatheka kuyeza kulemera kwa mkuwa+ ndi zitsulo+ chifukwa n’zochuluka kwambiri. Ndakonzanso matabwa ndi miyala, koma udzawonjezerapo zina.

  • Yeremiya 52:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Koma panalibe amene anayeza kulemera kwa mkuwa wa zipilala ziwiri zija,+ chosungiramo madzi chimodzi chija,+ ng’ombe zamkuwa 12+ zija ndi zotengera zokhala ndi mawilo zimene Mfumu Solomo inapangira nyumba ya Yehova.+ Palibe amene anayeza kulemera kwa mkuwa wa ziwiya zonsezi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena