1 Mafumu 7:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno Hiramu anaika zipilala+ zija pakhonde+ la kachisi. Chipilala chimodzi anachiika mbali ya kudzanja lamanja n’kuchitcha Yakini. Chipilala china anachiika mbali ya kumanzere n’kuchitcha Boazi.
21 Ndiyeno Hiramu anaika zipilala+ zija pakhonde+ la kachisi. Chipilala chimodzi anachiika mbali ya kudzanja lamanja n’kuchitcha Yakini. Chipilala china anachiika mbali ya kumanzere n’kuchitcha Boazi.