2 Mbiri 6:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Inu Yehova Mulungu, musakane wodzozedwa wanu.+ Musaiwale kukoma mtima kosatha kumene munasonyeza Davide mtumiki wanu.”+
42 Inu Yehova Mulungu, musakane wodzozedwa wanu.+ Musaiwale kukoma mtima kosatha kumene munasonyeza Davide mtumiki wanu.”+