1 Mafumu 1:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Kumeneko, wansembe Zadoki ndi mneneri Natani akam’dzoze+ kukhala mfumu ya Isiraeli. Ndiyeno mukalize lipenga+ ndi kunena kuti, ‘Mfumu Solomo ikhale ndi moyo wautali!’+ Salimo 18:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Iye akuchita ntchito zazikulu za chipulumutso kwa mfumu yake,+Ndipo akusonyeza kukoma mtima kosatha kwa wodzozedwa wake,+kwa Davide ndi mbewu yake mpaka kalekale.+
34 Kumeneko, wansembe Zadoki ndi mneneri Natani akam’dzoze+ kukhala mfumu ya Isiraeli. Ndiyeno mukalize lipenga+ ndi kunena kuti, ‘Mfumu Solomo ikhale ndi moyo wautali!’+
50 Iye akuchita ntchito zazikulu za chipulumutso kwa mfumu yake,+Ndipo akusonyeza kukoma mtima kosatha kwa wodzozedwa wake,+kwa Davide ndi mbewu yake mpaka kalekale.+