Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 10:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Ndiyeno Samueli anauza anthu onsewo kuti: “Kodi mwaona amene Yehova wam’sankha,+ kuti palibe aliyense pakati pa anthu onse wofanana naye?” Pamenepo anthu onsewo anayamba kufuula, kuti: “Mfumu ikhale ndi moyo wautali!”+

  • 2 Mafumu 11:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Kenako anatulutsa mwana+ wa mfumu uja. Atatero anamuveka chisoti chachifumu+ n’kuika mpukutu wa Chilamulo cha Mulungu pamutu pake.+ Chotero anamulonga ufumu+ n’kumudzoza.+ Ndiyeno anayamba kuwomba m’manja+ n’kumanena kuti: “Mfumu ikhale ndi moyo wautali!”+

  • 2 Mbiri 23:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Kenako anatulutsa mwana wa mfumu uja.+ Atatero anamuveka chisoti chachifumu+ n’kuika mpukutu wa Chilamulo cha Mulungu pamutu pake.+ Chotero anamulonga ufumu, ndipo Yehoyada ndi ana ake anamudzoza+ n’kuyamba kunena kuti: “Mfumu ikhale ndi moyo wautali!”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena