Ekisodo 25:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chivundikirocho+ uchiike pamwamba pa Likasalo, ndipo m’Likasamo uikemo umboni umene ndidzakupatsa. Ekisodo 31:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno atamaliza kulankhula naye paphiri la Sinai, anapatsa Mose miyala iwiri yosema ya Umboni,+ miyala yolembedwapo mawu ndi chala cha Mulungu.+
21 Chivundikirocho+ uchiike pamwamba pa Likasalo, ndipo m’Likasamo uikemo umboni umene ndidzakupatsa.
18 Ndiyeno atamaliza kulankhula naye paphiri la Sinai, anapatsa Mose miyala iwiri yosema ya Umboni,+ miyala yolembedwapo mawu ndi chala cha Mulungu.+