Ekisodo 25:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chivundikirocho+ udzachiike pa Likasalo, ndipo mu Likasamo udzaikemo Umboni umene ndidzakupatse.