-
Aheberi 9:4, 5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Mmenemu munali chiwaya chagolide chofukizira nsembe+ ndi likasa la pangano+ lokutidwa ndi golide.+ Mulikasamo munali mtsuko wagolide wokhala ndi mana,+ ndodo ya Aroni imene inaphuka ija+ komanso miyala yosema+ ya pangano. 5 Pamwamba pa likasalo panali akerubi aulemerero amene zithunzithunzi zawo zinkafika pachivundikiro.*+ Koma ino si nthawi yofotokoza zinthu zimenezi mwatsatanetsatane.
-