Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 25:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Mupangenso akerubi awiri agolide. Akhale osula ndipo muwaike kumapeto onse awiri a chivundikirocho.+

  • Ekisodo 25:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Ine ndidzaonekera kwa iwe pamenepo nʼkulankhula nawe kuchokera pamwamba pa chivundikirocho.+ Ndidzakuuza malamulo onse oti ukauze Aisiraeli kuchokera pakati pa akerubi awiriwo, amene ali pamwamba pa likasa la Umboni.

  • Numeri 7:89
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 89 Nthawi zonse Mose akalowa mʼchihema chokumanako kukalankhula ndi Mulungu,+ ankamva mawu akulankhula naye kuchokera pachivundikiro+ chimene chinali pamwamba pa likasa la Umboni, pakati pa akerubi+ awiri. Mulungu ankalankhula naye mwa njira imeneyi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena