1 Samueli 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho anatumiza anthu ku Silo kukatenga likasa la pangano la Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, amene amakhala pamwamba* pa akerubi.+ Ana awiri a Eli, Hofeni ndi Pinihasi,+ analinso komweko limodzi ndi likasa la pangano la Mulungu woona. Aheberi 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamwamba pa likasalo panali akerubi aulemerero amene zithunzithunzi zawo zinkafika pachivundikiro.*+ Koma ino si nthawi yofotokoza zinthu zimenezi mwatsatanetsatane.
4 Choncho anatumiza anthu ku Silo kukatenga likasa la pangano la Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, amene amakhala pamwamba* pa akerubi.+ Ana awiri a Eli, Hofeni ndi Pinihasi,+ analinso komweko limodzi ndi likasa la pangano la Mulungu woona.
5 Pamwamba pa likasalo panali akerubi aulemerero amene zithunzithunzi zawo zinkafika pachivundikiro.*+ Koma ino si nthawi yofotokoza zinthu zimenezi mwatsatanetsatane.