Ekisodo 25:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ine ndidzaonekera kwa iwe pamenepo nʼkulankhula nawe kuchokera pamwamba pa chivundikirocho.+ Ndidzakuuza malamulo onse oti ukauze Aisiraeli kuchokera pakati pa akerubi awiriwo, amene ali pamwamba pa likasa la Umboni. Ekisodo 37:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anapanga chivundikiro chagolide woyenga bwino+ masentimita 110 mulitali ndi masentimita 70 mulifupi.+
22 Ine ndidzaonekera kwa iwe pamenepo nʼkulankhula nawe kuchokera pamwamba pa chivundikirocho.+ Ndidzakuuza malamulo onse oti ukauze Aisiraeli kuchokera pakati pa akerubi awiriwo, amene ali pamwamba pa likasa la Umboni.
6 Anapanga chivundikiro chagolide woyenga bwino+ masentimita 110 mulitali ndi masentimita 70 mulifupi.+