14 Ndiyeno azitenga ena mwa magazi a ngʼombe yamphongoyo+ nʼkuwadontheza ndi chala chake patsogolo pa chivundikiro, mbali ya kumʼmawa. Azidontheza magaziwo ndi chala chake maulendo 7 patsogolo pa chivundikirocho.+
11 Atatero, Davide anapatsa Solomo mwana wake mapulani akamangidwe+ ka khonde+ ndi nyumba zake, zipinda zake zosungiramo katundu, zipinda zake zapadenga, zipinda zake zamkati ndiponso nyumba yokhalamo chivundikiro chophimbira machimo.+