-
Numeri 4:19, 20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Koma uchite izi kuti iwo asaphedwe chifukwa choyandikira zinthu zopatulika koposa:+ Aroni ndi ana ake azilowa mʼchihemacho, ndipo munthu aliyense azimugawira ntchito ndi katundu woti anyamule. 20 Ana a Kohatiwo asadzalowe kuti akaone zinthu zopatulikazo ngakhale pangʼono pokha chifukwa akadzatero adzafa.”+
-