-
Ekisodo 19:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Tsopano Yehova anauza Mose kuti: “Tsika ukachenjeze anthuwo kuti asayese kudumpha malire kufika kwa Yehova kuti amuone, chifukwa onse ochita zimenezi adzafa.
-