1 Samueli 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Chotero Mulungu anakantha anthu a ku Beti-semesi,+ chifukwa anayang’anitsitsa likasa la Yehova. Anakantha anthu 70 [[anthu 50,000]]* pakati pawo, ndipo anthu anayamba kulira chifukwa Yehova anakantha anthuwo koopsa.+
19 Chotero Mulungu anakantha anthu a ku Beti-semesi,+ chifukwa anayang’anitsitsa likasa la Yehova. Anakantha anthu 70 [[anthu 50,000]]* pakati pawo, ndipo anthu anayamba kulira chifukwa Yehova anakantha anthuwo koopsa.+