Ekisodo 37:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anapanga chivundikiro chagolide woyenga bwino+ masentimita 110 mulitali ndi masentimita 70 mulifupi.+ 1 Mbiri 28:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Atatero, Davide anapatsa Solomo mwana wake mapulani akamangidwe+ ka khonde+ ndi nyumba zake, zipinda zake zosungiramo katundu, zipinda zake zapadenga, zipinda zake zamkati ndiponso nyumba yokhalamo chivundikiro chophimbira machimo.+
6 Anapanga chivundikiro chagolide woyenga bwino+ masentimita 110 mulitali ndi masentimita 70 mulifupi.+
11 Atatero, Davide anapatsa Solomo mwana wake mapulani akamangidwe+ ka khonde+ ndi nyumba zake, zipinda zake zosungiramo katundu, zipinda zake zapadenga, zipinda zake zamkati ndiponso nyumba yokhalamo chivundikiro chophimbira machimo.+