1 Mafumu 1:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Atatero anthuwo anayamba kumulondola ndipo anali kuimba zitoliro+ ndi kusangalala kwambiri,+ moti nthaka+ inang’ambika chifukwa cha phokoso lawo. Salimo 47:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Ombani m’manja anthu nonsenu.+Fuulirani Mulungu mokondwera chifukwa chakuti wapambana.+
40 Atatero anthuwo anayamba kumulondola ndipo anali kuimba zitoliro+ ndi kusangalala kwambiri,+ moti nthaka+ inang’ambika chifukwa cha phokoso lawo.