1 Mafumu 1:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Kumeneko, wansembe Zadoki ndi mneneri Natani akam’dzoze+ kukhala mfumu ya Isiraeli. Ndiyeno mukalize lipenga+ ndi kunena kuti, ‘Mfumu Solomo ikhale ndi moyo wautali!’+ Salimo 72:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye akhale ndi moyo wautali,+ ndipo apatsidwe wina mwa golide wa ku Sheba.+Nthawi zonse anthu azimupempherera.Adalitsike tsiku lililonse.+ Mlaliki 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Dziko iwe, ndiwe wodala ngati mfumu yako ili mwana wochokera ku banja lachifumu, ndipo akalonga ako amadya pa nthawi yake kuti akhale amphamvu, osati kumangomwa mopitirira muyezo.+
34 Kumeneko, wansembe Zadoki ndi mneneri Natani akam’dzoze+ kukhala mfumu ya Isiraeli. Ndiyeno mukalize lipenga+ ndi kunena kuti, ‘Mfumu Solomo ikhale ndi moyo wautali!’+
15 Iye akhale ndi moyo wautali,+ ndipo apatsidwe wina mwa golide wa ku Sheba.+Nthawi zonse anthu azimupempherera.Adalitsike tsiku lililonse.+
17 Dziko iwe, ndiwe wodala ngati mfumu yako ili mwana wochokera ku banja lachifumu, ndipo akalonga ako amadya pa nthawi yake kuti akhale amphamvu, osati kumangomwa mopitirira muyezo.+