Salimo 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mfumuyo inakupemphani moyo. Ndipo munaipatsadi,+Munaipatsa masiku ochuluka kuti ikhale mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+ Yohane 14:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kwatsala kanthawi pang’ono ndipo dziko silidzandionanso.+ Koma inu mudzandiona,+ chifukwa ndili ndi moyo, inunso mudzakhala ndi moyo.+ 1 Yohane 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 (Ife taona ndipo tikuchitira umboni+ ndi kunena kwa inu za moyo wosatha+ umene unachokera kwa Atate ndipo unaonetsedwa kwa ife.)+ Chivumbulutso 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 ndiponso wamoyo.+ Ndinali wakufa,+ koma taona, ndili ndi moyo kwamuyaya,+ ndipo ndili ndi makiyi a imfa+ ndi a Manda.*+
4 Mfumuyo inakupemphani moyo. Ndipo munaipatsadi,+Munaipatsa masiku ochuluka kuti ikhale mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+
19 Kwatsala kanthawi pang’ono ndipo dziko silidzandionanso.+ Koma inu mudzandiona,+ chifukwa ndili ndi moyo, inunso mudzakhala ndi moyo.+
2 (Ife taona ndipo tikuchitira umboni+ ndi kunena kwa inu za moyo wosatha+ umene unachokera kwa Atate ndipo unaonetsedwa kwa ife.)+
18 ndiponso wamoyo.+ Ndinali wakufa,+ koma taona, ndili ndi moyo kwamuyaya,+ ndipo ndili ndi makiyi a imfa+ ndi a Manda.*+