Salimo 89:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndidzakhazikitsa mbewu yake kwamuyaya,+Ndipo mpando wake wachifumu udzakhalapo kwa masiku ochuluka ngati masiku a kumwamba.+ Salimo 91:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndidzamukhutiritsa ndi masiku ambiri,+Ndipo ndidzamuonetsa chipulumutso changa.”+
29 Ndidzakhazikitsa mbewu yake kwamuyaya,+Ndipo mpando wake wachifumu udzakhalapo kwa masiku ochuluka ngati masiku a kumwamba.+