Salimo 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mfumuyo inakupemphani moyo. Ndipo munaipatsadi,+Munaipatsa masiku ochuluka kuti ikhale mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+ Salimo 36:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti inu ndinu kasupe wa moyo.+Chifukwa cha kuwala kochokera kwa inu, tikuona kuwala.+ Miyambo 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ukatero, udzakhala ndi masiku ochuluka, moyo wazaka zambiri,+ ndi mtendere.+
4 Mfumuyo inakupemphani moyo. Ndipo munaipatsadi,+Munaipatsa masiku ochuluka kuti ikhale mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+