Yohane 16:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kwa kanthawi simudzandionanso,+ ndipo kwa kanthawi mudzandiona.” Yohane 17:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Atate, ine ndikufuna kuti amene mwandipatsawa adzakhale limodzi ndi ine kumene ine ndidzakhale,+ kuti adzaone ulemerero wanga umene inu mwandipatsa, chifukwa munandikonda musanayale maziko+ a dziko.+
24 Atate, ine ndikufuna kuti amene mwandipatsawa adzakhale limodzi ndi ine kumene ine ndidzakhale,+ kuti adzaone ulemerero wanga umene inu mwandipatsa, chifukwa munandikonda musanayale maziko+ a dziko.+