Yohane 7:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Pamenepo Yesu anati: “Ndikhala nanube kanthawi pang’ono ndisanapite kwa iye amene anandituma.+ Yohane 14:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kwatsala kanthawi pang’ono ndipo dziko silidzandionanso.+ Koma inu mudzandiona,+ chifukwa ndili ndi moyo, inunso mudzakhala ndi moyo.+
19 Kwatsala kanthawi pang’ono ndipo dziko silidzandionanso.+ Koma inu mudzandiona,+ chifukwa ndili ndi moyo, inunso mudzakhala ndi moyo.+