1 Mafumu 14:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Nthawi iliyonse imene mfumuyo ikupita kunyumba ya Yehova, asilikali othamangawo ankanyamula zishangozo, ndipo kenako ankazibwezera kuchipinda cha alonda.+ 2 Mbiri 24:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho anamuika m’manda a mafumu mu Mzinda wa Davide,+ chifukwa anachita zabwino mu Isiraeli+ ndiponso kwa Mulungu woona ndi nyumba Yake.
28 Nthawi iliyonse imene mfumuyo ikupita kunyumba ya Yehova, asilikali othamangawo ankanyamula zishangozo, ndipo kenako ankazibwezera kuchipinda cha alonda.+
16 Choncho anamuika m’manda a mafumu mu Mzinda wa Davide,+ chifukwa anachita zabwino mu Isiraeli+ ndiponso kwa Mulungu woona ndi nyumba Yake.