Deuteronomo 29:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pamenepo anthu adzanena kuti, ‘N’chifukwa chakuti anataya pangano+ la Yehova Mulungu wa makolo awo, limene anapangana nawo pamene anali kuwatulutsa m’dziko la Iguputo.+ 2 Mbiri 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndipo adzati, ‘N’chifukwa chakuti anasiya Yehova+ Mulungu wa makolo awo amene anawatulutsa m’dziko la Iguputo.+ M’malomwake anatenga milungu ina+ n’kumaigwadira ndi kuitumikira.+ N’chifukwa chake iye anawabweretsera tsoka lonseli.’”+
25 Pamenepo anthu adzanena kuti, ‘N’chifukwa chakuti anataya pangano+ la Yehova Mulungu wa makolo awo, limene anapangana nawo pamene anali kuwatulutsa m’dziko la Iguputo.+
22 Ndipo adzati, ‘N’chifukwa chakuti anasiya Yehova+ Mulungu wa makolo awo amene anawatulutsa m’dziko la Iguputo.+ M’malomwake anatenga milungu ina+ n’kumaigwadira ndi kuitumikira.+ N’chifukwa chake iye anawabweretsera tsoka lonseli.’”+