Ekisodo 12:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Ndipo pa tsiku limeneli, Yehova anatulutsa ana a Isiraeli malinga ndi makamu awo+ m’dziko la Iguputo. Deuteronomo 29:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pamenepo anthu adzanena kuti, ‘N’chifukwa chakuti anataya pangano+ la Yehova Mulungu wa makolo awo, limene anapangana nawo pamene anali kuwatulutsa m’dziko la Iguputo.+
51 Ndipo pa tsiku limeneli, Yehova anatulutsa ana a Isiraeli malinga ndi makamu awo+ m’dziko la Iguputo.
25 Pamenepo anthu adzanena kuti, ‘N’chifukwa chakuti anataya pangano+ la Yehova Mulungu wa makolo awo, limene anapangana nawo pamene anali kuwatulutsa m’dziko la Iguputo.+