2 Mbiri 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Solomo anaiyankha mfumukaziyo mafunso ake onse.+ Panalibe chimene Solomo analephera kuyankha.+ Miyambo 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Munthu wanzeru amamvetsera ndi kuphunzira malangizo owonjezereka,+ ndipo munthu womvetsa zinthu ndi amene amapeza nzeru zoyendetsera moyo wake,+ Miyambo 13:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Munthu woyenda ndi anthu anzeru adzakhala wanzeru,+ koma wochita zinthu ndi anthu opusa adzapeza mavuto.+
5 Munthu wanzeru amamvetsera ndi kuphunzira malangizo owonjezereka,+ ndipo munthu womvetsa zinthu ndi amene amapeza nzeru zoyendetsera moyo wake,+
20 Munthu woyenda ndi anthu anzeru adzakhala wanzeru,+ koma wochita zinthu ndi anthu opusa adzapeza mavuto.+