Salimo 18:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ananditenga ndi kundiika pamalo otakasuka.+Anandipulumutsa chifukwa anakondwera nane.+