2 Mbiri 9:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Solomo anakhala ndi makola 4,000 a mahatchi.+ Analinso ndi magaleta+ ndi mahatchi ankhondo okwana 12,000. Zimenezi anali kuzisunga m’mizinda yosungiramo magaleta+ ndiponso pafupi ndi mfumuyo ku Yerusalemu.
25 Solomo anakhala ndi makola 4,000 a mahatchi.+ Analinso ndi magaleta+ ndi mahatchi ankhondo okwana 12,000. Zimenezi anali kuzisunga m’mizinda yosungiramo magaleta+ ndiponso pafupi ndi mfumuyo ku Yerusalemu.