1 Mafumu 10:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Solomo anali kusonkhanitsa magaleta ambiri ndi mahatchi ankhondo, ndipo anakhala ndi magaleta 1,400 ndi mahatchi ankhondo 12,000.+ Zimenezi anali kuzisunga m’mizinda yake yosungiramo magaleta ndiponso pafupi ndi mfumuyo ku Yerusalemu.+
26 Solomo anali kusonkhanitsa magaleta ambiri ndi mahatchi ankhondo, ndipo anakhala ndi magaleta 1,400 ndi mahatchi ankhondo 12,000.+ Zimenezi anali kuzisunga m’mizinda yake yosungiramo magaleta ndiponso pafupi ndi mfumuyo ku Yerusalemu.+