Deuteronomo 17:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma asadzichulukitsire mahatchi+ kapena kuchititsa anthu kubwerera ku Iguputo kuti akakhale ndi mahatchi ochuluka+ pakuti Yehova wakuuzani kuti, ‘Musabwererenso kudzera njira iyi.’ 1 Mafumu 4:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Solomo anali ndi makola 40,000 a mahatchi+ okoka magaleta ake,+ ndi amuna 12,000 okwera pamahatchi.
16 Koma asadzichulukitsire mahatchi+ kapena kuchititsa anthu kubwerera ku Iguputo kuti akakhale ndi mahatchi ochuluka+ pakuti Yehova wakuuzani kuti, ‘Musabwererenso kudzera njira iyi.’
26 Solomo anali ndi makola 40,000 a mahatchi+ okoka magaleta ake,+ ndi amuna 12,000 okwera pamahatchi.