2 Mbiri 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiyeno Solomo anali kusonkhanitsa magaleta* ndi mahatchi* ankhondo, moti anakhala ndi magaleta 1,400 ndi mahatchi ankhondo 12,000.+ Zimenezi anali kuzisunga m’mizinda yosungiramo magaleta+ ndiponso pafupi ndi mfumuyo ku Yerusalemu.
14 Ndiyeno Solomo anali kusonkhanitsa magaleta* ndi mahatchi* ankhondo, moti anakhala ndi magaleta 1,400 ndi mahatchi ankhondo 12,000.+ Zimenezi anali kuzisunga m’mizinda yosungiramo magaleta+ ndiponso pafupi ndi mfumuyo ku Yerusalemu.