Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 8:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Anamanganso Baalati+ ndi mizinda yonse yosungirako zinthu imene inakhala ya Solomo, mizinda yonse yosungirako magaleta,+ mizinda yonse ya amuna okwera pamahatchi,+ ndi chilichonse chimene iye anakonda+ kumanga ku Yerusalemu, ku Lebanoni,+ ndi m’dziko lonse limene ankalamulira.

  • 2 Mbiri 9:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Solomo anakhala ndi makola 4,000 a mahatchi.+ Analinso ndi magaleta+ ndi mahatchi ankhondo okwana 12,000. Zimenezi anali kuzisunga m’mizinda yosungiramo magaleta+ ndiponso pafupi ndi mfumuyo ku Yerusalemu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena