2 Mbiri 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mfumuyo inachititsa kuti ku Yerusalemu siliva ndi golide akhale wochuluka kwambiri ngati miyala,+ ndiponso kuti matabwa a mkungudza akhale ochuluka kwambiri ngati mitengo yamkuyu+ ya ku Sefela.+
15 Mfumuyo inachititsa kuti ku Yerusalemu siliva ndi golide akhale wochuluka kwambiri ngati miyala,+ ndiponso kuti matabwa a mkungudza akhale ochuluka kwambiri ngati mitengo yamkuyu+ ya ku Sefela.+