2 Mafumu 16:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ahazi anali ndi zaka 20 pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 16. Iye sanachite zoyenera pamaso pa Yehova Mulungu wake monga anachitira Davide kholo lake.+ 2 Mafumu 16:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pomalizira pake, Ahazi anagona pamodzi ndi makolo ake ndipo anaikidwa m’manda mu Mzinda wa Davide+ pamodzi ndi makolo ake. Kenako Hezekiya+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.
2 Ahazi anali ndi zaka 20 pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 16. Iye sanachite zoyenera pamaso pa Yehova Mulungu wake monga anachitira Davide kholo lake.+
20 Pomalizira pake, Ahazi anagona pamodzi ndi makolo ake ndipo anaikidwa m’manda mu Mzinda wa Davide+ pamodzi ndi makolo ake. Kenako Hezekiya+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.