Nehemiya 13:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Hafu ya ana awo aamuna anali kulankhula Chiasidodi ndipo palibe amene ankatha kulankhula Chiyuda,+ koma anali kulankhula chinenero cha anthu ena. Machitidwe 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 (Atamva kuti akulankhula nawo m’Chiheberi,+ onse anangoti zii osanena kanthu, ndipo iye anati:)
24 Hafu ya ana awo aamuna anali kulankhula Chiasidodi ndipo palibe amene ankatha kulankhula Chiyuda,+ koma anali kulankhula chinenero cha anthu ena.