Genesis 37:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Pambuyo pake, Rubeni anabwerera kuchitsime kuja, koma anakapeza kuti Yosefe mulibe m’chitsimemo. Ataona choncho, anang’amba zovala zake.+ 2 Mafumu 22:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mfumuyo itangomva mawu a m’buku la chilamulolo, nthawi yomweyo inang’amba zovala zake.+
29 Pambuyo pake, Rubeni anabwerera kuchitsime kuja, koma anakapeza kuti Yosefe mulibe m’chitsimemo. Ataona choncho, anang’amba zovala zake.+