Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 44:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Zitatero, iwo anang’amba zovala zawo.+ Kenako aliyense anakwezanso thumba lake pabulu wake n’kubwerera kumzinda kuja.

  • 2 Samueli 1:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Davide atamva zimenezi anagwira zovala zake ndi kuzing’amba.+ Nawonso amuna onse amene anali ndi Davide anang’amba zovala zawo.

  • 2 Mbiri 34:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Mfumuyo itangomva mawu a chilamulowo, nthawi yomweyo inang’amba zovala zake.+

  • Yeremiya 36:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Iwo sanachite mantha+ ndipo mfumu ndi atumiki ake onse amene anali kumvetsera mawu amenewa sanang’ambe zovala zawo.+

  • Yoweli 2:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ng’ambani mitima yanu+ osati zovala zanu+ ndipo bwererani kwa Yehova Mulungu wanu pakuti iye ndi wachisomo, wachifundo,+ wosakwiya msanga+ ndiponso wodzaza ndi kukoma mtima kosatha.+ Ndithu, iye adzakumverani chisoni chifukwa cha tsokalo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena