Salimo 36:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Uchimo ukulankhula mumtima mwa munthu woipa.+Maso ake saona chifukwa choopera Mulungu.+