Yoswa 10:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Zitatero, Yoswa ndi Aisiraeli onse amene anali naye anachoka ku Makeda n’kupita ku Libina+ komwe anakachitako nkhondo. 2 Mafumu 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma Aedomu anapitirizabe kugalukira Yuda mpaka lero. Inalinso nthawi imeneyi pamene Libina+ anagalukira Yuda. Yesaya 37:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Rabisake+ anali atamva kuti mfumu ya Asuri yachoka ku Lakisi,+ choncho anabwerera kwa mfumuyo n’kukaipeza ikumenyana ndi Libina.+
29 Zitatero, Yoswa ndi Aisiraeli onse amene anali naye anachoka ku Makeda n’kupita ku Libina+ komwe anakachitako nkhondo.
22 Koma Aedomu anapitirizabe kugalukira Yuda mpaka lero. Inalinso nthawi imeneyi pamene Libina+ anagalukira Yuda.
8 Rabisake+ anali atamva kuti mfumu ya Asuri yachoka ku Lakisi,+ choncho anabwerera kwa mfumuyo n’kukaipeza ikumenyana ndi Libina.+